Genesis 37:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+ 1 Mafumu 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+ 2 Mafumu 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mfumuyo itamva mawu a mayiyo, nthawi yomweyo inang’amba+ zovala zake, ndipo pamene inali kuyendabe pamwamba pa khomalo, anthu anaona kuti inali itavala chiguduli* mkati. Esitere 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moredekai+ anadziwa zonse zimene zinachitika.+ Choncho anang’amba zovala zake ndi kuvala chiguduli*+ ndipo anadzithira phulusa+ ndi kutuluka kupita pakati pa mzinda. Ndiyeno anayamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima.+ Salimo 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+ Yesaya 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+
34 Pamenepo Yakobo anang’amba zovala zake, n’kuvala chiguduli* m’chiuno mwake, ndipo anamulira mwana wake masiku ambiri.+
27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+
30 Mfumuyo itamva mawu a mayiyo, nthawi yomweyo inang’amba+ zovala zake, ndipo pamene inali kuyendabe pamwamba pa khomalo, anthu anaona kuti inali itavala chiguduli* mkati.
4 Moredekai+ anadziwa zonse zimene zinachitika.+ Choncho anang’amba zovala zake ndi kuvala chiguduli*+ ndipo anadzithira phulusa+ ndi kutuluka kupita pakati pa mzinda. Ndiyeno anayamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima.+
13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+
12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+