Ezekieli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma iwe mwana wa munthu, buula mwamantha.+ Ubuule pamaso pawo mowawidwa mtima.+ Mika 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa cha zimenezi ndidzalira ndi kufuula.+ Ndidzayenda wopanda nsapato komanso wosavala.+ Ndidzalira ngati mimbulu ndi kumva chisoni ngati nthiwatiwa zazikazi.
8 Chifukwa cha zimenezi ndidzalira ndi kufuula.+ Ndidzayenda wopanda nsapato komanso wosavala.+ Ndidzalira ngati mimbulu ndi kumva chisoni ngati nthiwatiwa zazikazi.