Salimo 69:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,+Ndipo chititsani miyendo* yawo kunjenjemera mosalekeza.+ Ezekieli 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.”
7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.”