Yesaya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+ Yohane 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo,+ kuti asamaone ndi maso awowo, asazindikire ndi mitima yawo ndi kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+ Machitidwe 28:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mzimuwo unati, ‘Pita ukauze anthu awa kuti: “Kumva mudzamva ndithu, koma osazindikira ngakhale pang’ono. Kupenya mudzapenya ndithu, koma osaona ngakhale pang’ono.+ 2 Akorinto 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+
9 Iye anapitiriza kunena kuti: “Pita ukauze anthu awa kuti, ‘Imvani mobwerezabwereza anthu inu, koma musamvetsetse. Onani mobwerezabwereza, koma musazindikire chilichonse.’+
40 “Wachititsa khungu maso awo ndipo waumitsa mitima yawo,+ kuti asamaone ndi maso awowo, asazindikire ndi mitima yawo ndi kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”+
26 Mzimuwo unati, ‘Pita ukauze anthu awa kuti: “Kumva mudzamva ndithu, koma osazindikira ngakhale pang’ono. Kupenya mudzapenya ndithu, koma osaona ngakhale pang’ono.+
14 Ndipo maganizo awo anachita khungu.+ Pakuti mpaka lero, nsaluyo imakhalabe yophimba powerenga pangano lakale,+ chifukwa imachotsedwa kudzera mwa Khristu basi.+