Deuteronomo 28:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Pakati pa mitundu imeneyo sudzakhala mwamtendere,+ ndipo sudzapeza malo oti phazi lako liponde kuti lipumulirepo. Kumeneko, Yehova adzakupatsa mtima wachinthenthe,+ adzachititsa maso ako+ khungu ndipo adzakutayitsa mtima. Ezekieli 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.” Aroma 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Maso awo achite mdima kuti asaone, ndipo weramitsani msana wawo nthawi zonse.”+
65 Pakati pa mitundu imeneyo sudzakhala mwamtendere,+ ndipo sudzapeza malo oti phazi lako liponde kuti lipumulirepo. Kumeneko, Yehova adzakupatsa mtima wachinthenthe,+ adzachititsa maso ako+ khungu ndipo adzakutayitsa mtima.
7 Atakugwira dzanja ndi kukutsamira ngati ndodo yoyendera, unaphwanyika+ ndipo unachititsa kuti miyendo* yawo ikhale yagwedegwede,+ zimene zinawachititsa kuti athyole+ phewa lawo.”