Salimo 69:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,+Ndipo chititsani miyendo* yawo kunjenjemera mosalekeza.+ Ezekieli 21:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma iwe mwana wa munthu, buula mwamantha.+ Ubuule pamaso pawo mowawidwa mtima.+