Genesis 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+ 1 Mafumu 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+ 2 Mafumu 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mfumu Hezekiya+ itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake+ n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+
29 Pambuyo pake, Rubeni anabwerera kuchitsime kuja, koma anakapeza kuti Yosefe mulibe m’chitsimemo. Ataona choncho, anang’amba zovala zake.+
27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+
19 Mfumu Hezekiya+ itangomva zimenezi, nthawi yomweyo inang’amba zovala zake+ n’kuvala chiguduli.+ Kenako inapita m’nyumba ya Yehova.+