Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 8:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndiyeno Nehemiya+ amene ndiye Tirisata+ komanso Ezara+ wansembe, wokopera Malemba, ndi Alevi amene anali kupereka malangizo kwa anthu, anauza anthuwo kuti: “Lero ndi tsiku lopatulika kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musakhale achisoni ndipo musalire.”+ Ananena zimenezi chifukwa anthu onse anali kulira pamene anali kumvetsera mawu a m’chilamulo.+

  • Yesaya 15:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+

  • Yoweli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ansembe ndi atumiki a Yehova alire m’khonde mwa guwa lansembe+ ndipo anene kuti, ‘Inu Yehova, mverani chisoni anthu anu ndipo musachititse manyazi cholowa chanu+ kuti mitundu ya anthu iwalamulire. Anthu a mitundu ina asanene kuti: “Kodi Mulungu wawo ali kuti?”’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena