Ezara 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Izi n’zimene zinali m’kalata imene Mfumu Aritasasita inapatsa wansembe Ezara wokopera zinthu, wokopera+ mawu a malamulo a Yehova ndi malangizo ake kwa Aisiraeli:
11 Izi n’zimene zinali m’kalata imene Mfumu Aritasasita inapatsa wansembe Ezara wokopera zinthu, wokopera+ mawu a malamulo a Yehova ndi malangizo ake kwa Aisiraeli: