Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 3:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Ndiyeno Davide anauza Yowabu ndi anthu onse amene anali pamenepo kuti: “Ng’ambani zovala zanu+ ndipo muvale ziguduli*+ kuti mulire maliro a Abineri.” Ngakhale Mfumu Davide nayenso anayenda pambuyo pa chithatha cha Abineri.

  • 2 Mafumu 6:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Mfumuyo itamva mawu a mayiyo, nthawi yomweyo inang’amba+ zovala zake, ndipo pamene inali kuyendabe pamwamba pa khomalo, anthu anaona kuti inali itavala chiguduli* mkati.

  • Yesaya 24:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anthu akulira m’misewu chifukwa chosowa vinyo. Kusangalala konse kwatha. Chisangalalo cha dzikolo chachoka.+

  • Mateyu 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye anati: “Tsoka kwa iwe, Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida!+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli* ndi kukhala paphulusa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena