Danieli 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+ Yona 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Uthengawo utafika kwa mfumu ya Nineve,+ mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu ndi kuvula chovala chake chachifumu. Ndiyeno inavala chiguduli ndi kukhala paphulusa.+ Luka 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Tsoka iwe Korazini!+ Tsoka iwe Betsaida!+ Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika kumeneko zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu kumeneko akanalapa kalekale atavala ziguduli n’kukhala paphulusa.+
3 Ndinayang’ana+ kwa Yehova Mulungu woona kuti ndimufunefune mwa kupemphera,+ kumuchonderera, kusala kudya, kuvala ziguduli* ndi kudzithira phulusa.+
6 Uthengawo utafika kwa mfumu ya Nineve,+ mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu ndi kuvula chovala chake chachifumu. Ndiyeno inavala chiguduli ndi kukhala paphulusa.+
13 “Tsoka iwe Korazini!+ Tsoka iwe Betsaida!+ Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika kumeneko zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu kumeneko akanalapa kalekale atavala ziguduli n’kukhala paphulusa.+