Ezekieli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 osati kwa mitundu yambiri ya anthu olankhula chinenero chovuta kumva kapena a lilime lolemera, amene sungathe kumvetsetsa mawu awo.+ Ndikanakhala kuti ndinakutuma kwa anthu amenewo, akanakumvera.+
6 osati kwa mitundu yambiri ya anthu olankhula chinenero chovuta kumva kapena a lilime lolemera, amene sungathe kumvetsetsa mawu awo.+ Ndikanakhala kuti ndinakutuma kwa anthu amenewo, akanakumvera.+