Mateyu 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anati: “Tsoka kwa iwe, Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida!+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli* ndi kukhala paphulusa.+
21 Iye anati: “Tsoka kwa iwe, Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida!+ chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli* ndi kukhala paphulusa.+