Luka 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsoka kwa iwe Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida! Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanakhala kuti zinachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli nʼkukhala paphulusa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, ptsa. 16-17
13 Tsoka kwa iwe Korazini! Tsoka kwa iwe Betsaida! Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika mwa iwe zikanakhala kuti zinachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu akanakhala atalapa kalekale, atavala ziguduli nʼkukhala paphulusa.+