Luka 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Tsoka iwe Korazini!+ Tsoka iwe Betsaida!+ Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika kumeneko zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu kumeneko akanalapa kalekale atavala ziguduli n’kukhala paphulusa.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:13 Nsanja ya Olonda,7/1/1989, ptsa. 16-17
13 “Tsoka iwe Korazini!+ Tsoka iwe Betsaida!+ Chifukwa ntchito zamphamvu zimene zinachitika kumeneko zikanachitika ku Turo ndi ku Sidoni, anthu kumeneko akanalapa kalekale atavala ziguduli n’kukhala paphulusa.+