Yoswa 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+ 2 Samueli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Davide atamva zimenezi anagwira zovala zake ndi kuzing’amba.+ Nawonso amuna onse amene anali ndi Davide anang’amba zovala zawo.
6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+
11 Davide atamva zimenezi anagwira zovala zake ndi kuzing’amba.+ Nawonso amuna onse amene anali ndi Davide anang’amba zovala zawo.