Yesaya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu avala ziguduli mʼmisewu yake. Pamadenga awo komanso mʼmabwalo a mizinda yawo, onse akulira mofuula.Akulira nʼkumapita kumunsi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:3 Yesaya 1, ptsa. 193-194
3 Anthu avala ziguduli mʼmisewu yake. Pamadenga awo komanso mʼmabwalo a mizinda yawo, onse akulira mofuula.Akulira nʼkumapita kumunsi.+