Yesaya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:3 Yesaya 1, ptsa. 193-194
3 Anthu avala ziguduli+ m’misewu yake. Pamadenga*+ ake ndi m’mabwalo a mizinda yake, aliyense akufuula. Akulira n’kumapita kumunsi.+