Deuteronomo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo uzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu. Deuteronomo 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uzichitira Yehova Mulungu wako chikondwerero chimenecho masiku 7+ pamalo amene Yehova adzasankhe. Uzichita chikondwerero chimenecho chifukwa Yehova Mulungu wako adzakudalitsa+ pa zokolola zako zonse ndi pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita, ndipo iwe uzikhala wosangalala basi.+
14 Ndipo uzisangalala pa chikondwerero chimenecho,+ iweyo, mwana wako wamwamuna, mwana wako wamkazi, kapolo wako wamwamuna, kapolo wako wamkazi, Mlevi, mlendo wokhala pakati panu, mwana wamasiye ndi mkazi wamasiye, amene ali mumzinda wanu.
15 Uzichitira Yehova Mulungu wako chikondwerero chimenecho masiku 7+ pamalo amene Yehova adzasankhe. Uzichita chikondwerero chimenecho chifukwa Yehova Mulungu wako adzakudalitsa+ pa zokolola zako zonse ndi pa chilichonse chimene dzanja lako likuchita, ndipo iwe uzikhala wosangalala basi.+