Afilipi 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Nthawi zonse kondwerani mwa Ambuye.+ Ndibwerezanso, Kondwerani.+ 1 Atesalonika 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muzikhala okondwera nthawi zonse.+