1 Mafumu 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+ Salimo 69:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ndinavala ziguduli,Ndinakhala ngati mwambi kwa iwo.+ Chivumbulutso 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+
27 Ahabu atangomva mawu amenewa, anang’amba zovala zake n’kuvala chiguduli.+ Iye anayamba kusala kudya, kugona pachiguduli ndipo anali kuyenda mwachisoni.+
12 Atamatula chidindo cha 6, ndinaona kuti kunachitika chivomezi chachikulu. Dzuwa linada ngati chiguduli*+ choluka ndi ubweya wa mbuzi yakuda, ndipo mwezi wonse unafiira ngati magazi.+