-
Esitere 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako Hamani anauza Mfumu Ahasiwero kuti: “Pali mtundu wina wa anthu umene ukupezeka paliponse+ ndipo ukudzipatula pakati pa anthu m’zigawo zonse za ufumu wanu.+ Malamulo awo ndi osiyana ndi malamulo a anthu ena onse ndipo sakutsatira+ malamulo anu mfumu. Choncho si bwino kuti inu mfumu muwalekerere anthu amenewa.
-