Yobu 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndithu, ndalirira munthu amene zinthu sizikumuyendera bwino.+Moyo wanga walirira munthu wosauka.+ Salimo 69:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamene ndinavala ziguduli,Ndinakhala ngati mwambi kwa iwo.+