Salimo 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+ Aroma 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Sangalalani ndi anthu amene akusangalala.+ Lirani ndi anthu amene akulira.
13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+