Luka 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo ngati pakhomopo pali munthu wokonda mtendere, mtendere wanu udzakhala pa iye.+ Koma ngati palibe, udzabwerera kwa inu.+
6 Ndipo ngati pakhomopo pali munthu wokonda mtendere, mtendere wanu udzakhala pa iye.+ Koma ngati palibe, udzabwerera kwa inu.+