Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Yoswa ataona zimenezi anang’amba malaya ake. Kenako anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ patsogolo pa likasa la Yehova, mpaka madzulo. Anachita zimenezi pamodzi ndi akulu a Isiraeli, n’kumadzithira fumbi kumutu kwawo.+

  • Esitere 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Moredekai+ anadziwa zonse zimene zinachitika.+ Choncho anang’amba zovala zake ndi kuvala chiguduli*+ ndipo anadzithira phulusa+ ndi kutuluka kupita pakati pa mzinda. Ndiyeno anayamba kulira mofuula ndiponso mopwetekedwa mtima.+

  • Yobu 2:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Yobu anatenga phale loti azidzikanda nalo ndipo anali kukhala paphulusa.+

  • Yeremiya 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena