Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 1:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+

      Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+

      Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+

  • Maliro 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+

      Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.

      Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+

  • Amosi 5:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Choncho Yehova, Mulungu wa makamu, Yehova wanena kuti, ‘Padzamveka kulira m’mabwalo onse a mizinda+ yanu ndipo m’misewu yanu yonse anthu azidzanena kuti: “Aa! Aa!” Pamenepo adzaitana mlimi kuti alire+ ndiponso anthu odziwa kulira maliro kuti alire mokweza.’+

  • Luka 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Atayandikira pachipata cha mzindawo, anakumana ndi anthu atanyamula maliro.+ Womwalirayo anali mwana wamwamuna yekhayo+ kwa mayi ake. Komanso mayi akewo anali mkazi wamasiye. Khamu lalikulu ndithu la anthu ochokera mumzindawo linali limodzi ndi mayiwo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena