1 Mafumu 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pambuyo pa zimenezi, mwana wamwamuna wa mayi wa m’nyumbamo, anadwala. Matenda ake anakula kwambiri mpaka anamwalira.+ Luka 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yairo anachita zimenezi chifukwa mwana wake wamkazi wazaka pafupifupi 12, mwana yekhayo amene anali naye, anali pafupi kumwalira.+ Pamene anali kupita anthu ambiri anakhamukira komweko.+
17 Pambuyo pa zimenezi, mwana wamwamuna wa mayi wa m’nyumbamo, anadwala. Matenda ake anakula kwambiri mpaka anamwalira.+
42 Yairo anachita zimenezi chifukwa mwana wake wamkazi wazaka pafupifupi 12, mwana yekhayo amene anali naye, anali pafupi kumwalira.+ Pamene anali kupita anthu ambiri anakhamukira komweko.+