-
Luka 8:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Yairo anachita zimenezi chifukwa mwana wake wamkazi amene anali ndi zaka pafupifupi 12, mwana yekhayo amene anali naye, anali atatsala pangʼono kumwalira.
Pamene Yesu ankapita, anthu ambiri anamutsatira ndipo ankamupanikiza.
-