Luka 8:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Yairo anachita zimenezi chifukwa mwana wake wamkazi wazaka pafupifupi 12, mwana yekhayo amene anali naye, anali pafupi kumwalira.+ Pamene anali kupita anthu ambiri anakhamukira komweko.+
42 Yairo anachita zimenezi chifukwa mwana wake wamkazi wazaka pafupifupi 12, mwana yekhayo amene anali naye, anali pafupi kumwalira.+ Pamene anali kupita anthu ambiri anakhamukira komweko.+