Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+ Yeremiya 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo ngati simudzamvera mawu ake+ ndidzalira ndi kugwetsa misozi m’malo obisika chifukwa cha kunyada kwanu. Maso anga adzatulutsa misozi+ chifukwa chakuti nkhosa+ za Yehova zidzakhala zitagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina. Yeremiya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Ndiyeno uwauze kuti, ‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi usana ndipo asasiye kutulutsa misozi,+ pakuti pamveka kugunda kwakukulu ndipo namwali, mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Iye wawonongedwa ndi chilonda chachikulu cha mkwapulo chosachiritsika.+ Maliro 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mtima wa anthuwo wafuulira Yehova,+ iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni.+Gwetsa misozi ngati mtsinje usana ndi usiku.+Usapume. Mwana wa diso lako asaleke kulira.
9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+
17 Ndipo ngati simudzamvera mawu ake+ ndidzalira ndi kugwetsa misozi m’malo obisika chifukwa cha kunyada kwanu. Maso anga adzatulutsa misozi+ chifukwa chakuti nkhosa+ za Yehova zidzakhala zitagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.
17 “Ndiyeno uwauze kuti, ‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi usana ndipo asasiye kutulutsa misozi,+ pakuti pamveka kugunda kwakukulu ndipo namwali, mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Iye wawonongedwa ndi chilonda chachikulu cha mkwapulo chosachiritsika.+
18 Mtima wa anthuwo wafuulira Yehova,+ iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni.+Gwetsa misozi ngati mtsinje usana ndi usiku.+Usapume. Mwana wa diso lako asaleke kulira.