Yeremiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+ Maliro 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+ Maliro 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mtima wa anthuwo wafuulira Yehova,+ iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni.+Gwetsa misozi ngati mtsinje usana ndi usiku.+Usapume. Mwana wa diso lako asaleke kulira.
9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+
2 Iye akulira kwambiri usiku,+ ndipo misozi ikutsika pamasaya ake.+Pakati pa onse amene anali kumukonda, palibe amene akumutonthoza.+Anthu onse amene anali anzake amuchitira zachinyengo+ ndipo akhala adani ake.+
18 Mtima wa anthuwo wafuulira Yehova,+ iwe mpanda wa mwana wamkazi wa Ziyoni.+Gwetsa misozi ngati mtsinje usana ndi usiku.+Usapume. Mwana wa diso lako asaleke kulira.