Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndikanakonda kuti m’mutu mwanga mukhale madzi ambiri ndiponso kuti maso anga akhale magwero a misozi.+ Pamenepo ndikanalira usana ndi usiku chifukwa cha anthu ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga.+

  • Yeremiya 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo ngati simudzamvera mawu ake+ ndidzalira ndi kugwetsa misozi m’malo obisika chifukwa cha kunyada kwanu. Maso anga adzatulutsa misozi+ chifukwa chakuti nkhosa+ za Yehova zidzakhala zitagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.

  • Yeremiya 14:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “Ndiyeno uwauze kuti, ‘Maso anga atulutse misozi usiku ndi usana ndipo asasiye kutulutsa misozi,+ pakuti pamveka kugunda kwakukulu ndipo namwali, mwana wamkazi wa anthu anga wawonongedwa.+ Iye wawonongedwa ndi chilonda chachikulu cha mkwapulo chosachiritsika.+

  • Maliro 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndikulirira zinthu zimenezi ngati mkazi.+ Maso anga ine! Maso anga akutuluka misozi.+

      Pakuti wonditonthoza, munthu woti anditsitsimule, ali kutali ndi ine.

      Ana anga asiyidwa+ popanda thandizo, pakuti mdani wanga wadzitukumula.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena