Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+ Yeremiya 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova wanena kuti, ‘Mawu amveka ku Rama.+ Kwamveka kulira mofuula ndiponso momvetsa chisoni.+ Rakele+ akulirira ana ake.+ Iye wakana kutonthozedwa pamene akulirira ana ake,+ chifukwa ana akewo kulibenso.’”+
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
15 “Yehova wanena kuti, ‘Mawu amveka ku Rama.+ Kwamveka kulira mofuula ndiponso momvetsa chisoni.+ Rakele+ akulirira ana ake.+ Iye wakana kutonthozedwa pamene akulirira ana ake,+ chifukwa ana akewo kulibenso.’”+