Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 18:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti,

  • Yeremiya 40:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Awa ndi mawu amene Yehova anauza Yeremiya, pamene Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anamumasula ku Rama.+ Yeremiya anali womangidwa maunyolo a m’manja pamene Nebuzaradani anamutenga pakati pa anthu a ku Yerusalemu ndi a ku Yuda amene anali kupita ku ukapolo ku Babulo.+

  • Mateyu 2:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Mawu anamveka ku Rama,+ kulira ndi kubuma mofuula. Anali Rakele+ kulirira ana ake ndipo sanamve kumutonthoza, chifukwa ana akewo kunalibenso.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena