Yoswa 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunalinso Gibeoni,+ Rama, Beeroti, Oweruza 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anali kukhala patsinde pa mtengo wa kanjedza wa Debora, pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Ana a Isiraeli anali kupita kwa iye kukalandira zigamulo zochokera kwa Mulungu.
5 Iye anali kukhala patsinde pa mtengo wa kanjedza wa Debora, pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Ana a Isiraeli anali kupita kwa iye kukalandira zigamulo zochokera kwa Mulungu.