Genesis 28:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anachita mantha n’kunenanso kuti:+ “Malo ano ndi oopsa!+ Ndithu malo ano ndi nyumba ya Mulungu,+ ndiponso ndi khomo la kumwamba.” Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ Yeremiya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+ Amosi 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+
17 Iye anachita mantha n’kunenanso kuti:+ “Malo ano ndi oopsa!+ Ndithu malo ano ndi nyumba ya Mulungu,+ ndiponso ndi khomo la kumwamba.”
13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+
14 ‘Pa tsiku limene ndidzalanga Isiraeli+ chifukwa cha kupanduka kwake, ndidzaperekanso chiweruzo pamaguwa ansembe a ku Beteli+ ndipo nyanga za guwa lansembe zidzazulidwa ndi kugwa pansi.+