Oweruza 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anali kukhala patsinde pa mtengo wa kanjedza wa Debora, pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Ana a Isiraeli anali kupita kwa iye kukalandira zigamulo zochokera kwa Mulungu. Hoseya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+
5 Iye anali kukhala patsinde pa mtengo wa kanjedza wa Debora, pakati pa mzinda wa Rama+ ndi wa Beteli,+ m’dera lamapiri la Efuraimu. Ana a Isiraeli anali kupita kwa iye kukalandira zigamulo zochokera kwa Mulungu.
4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+