Genesis 32:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Atatero anauza Yakobo kuti: “Ndileke ndizipita, chifukwa kukucha tsopano.” Koma Yakobo anayankha kuti: “Sindikuleka, kufikira utandidalitsa choyamba.”+
26 Atatero anauza Yakobo kuti: “Ndileke ndizipita, chifukwa kukucha tsopano.” Koma Yakobo anayankha kuti: “Sindikuleka, kufikira utandidalitsa choyamba.”+