1 Mbiri 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano Yabezi anayamba kuitana Mulungu+ wa Isiraeli, kuti: “Mukandidalitsa+ ndi kukulitsa dziko langa,+ ndipo dzanja lanu+ likakhala nane, komanso mukanditeteza ku tsoka,+ kuti lisandivulaze,+ . . .” Choncho Mulungu anakwaniritsa zimene iye anapempha.+ Salimo 115:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+ Hoseya 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+
10 Tsopano Yabezi anayamba kuitana Mulungu+ wa Isiraeli, kuti: “Mukandidalitsa+ ndi kukulitsa dziko langa,+ ndipo dzanja lanu+ likakhala nane, komanso mukanditeteza ku tsoka,+ kuti lisandivulaze,+ . . .” Choncho Mulungu anakwaniritsa zimene iye anapempha.+
12 Yehova watikumbukira, ndipo adzapereka madalitso,+Adzadalitsa nyumba ya Isiraeli,+Adzadalitsa nyumba ya Aroni.+
4 Anapitiriza kulimbana ndi mngelo ndipo pamapeto pake anapambana.+ Analira pochonderera kuti amudalitse.”+ Mulungu anamupeza ku Beteli+ ndipo kumeneko Mulungu anayamba kulankhula nafe.+