Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 M’kupita kwa nthawi, anasamuka pamalopo n’kupita kudera lamapiri, kum’mawa kwa Beteli.+ Kumeneko iye anamanga hema wake. Beteli anali kumadzulo kwake ndipo Ai+ anali kum’mawa kwake. Kenako anamangira Yehova guwa lansembe,+ n’kuyamba kuitana pa dzina la Yehova.+

  • Salimo 55:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ine ndidzafuulira Mulungu.+

      Ndipo Yehova adzandipulumutsa.+

  • Salimo 99:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+

      Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+

      Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+

  • Yeremiya 33:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 ‘Mundiitane ndipo ndidzakuyankhani.+ Nthawi yomweyo ndidzakuuzani zinthu zazikulu ndi zovuta kuzimvetsa zimene simukuzidziwa.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena