Salimo 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+ Yesaya 48:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mwazimva.+ Onani zonsezo.+ Kodi simudzazifotokozera ena?+ Kuyambira panopa ine ndikukuuzani zinthu zatsopano. Ndakuuzani zinthu zobisika zimene simunali kuzidziwa.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+
6 Inuyo mwazimva.+ Onani zonsezo.+ Kodi simudzazifotokozera ena?+ Kuyambira panopa ine ndikukuuzani zinthu zatsopano. Ndakuuzani zinthu zobisika zimene simunali kuzidziwa.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+