Genesis 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kumeneko Isaki anamanga guwa lansembe n’kuitana pa dzina la Yehova.+ Anamanganso mahema ake,+ ndipo antchito ake anakumba chitsime kumeneko. Miyambo 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzina la Yehova ndi nsanja yolimba.+ Wolungama amathawira mmenemo ndipo amatetezedwa.+ Aroma 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti “aliyense amene adzaitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”+
25 Kumeneko Isaki anamanga guwa lansembe n’kuitana pa dzina la Yehova.+ Anamanganso mahema ake,+ ndipo antchito ake anakumba chitsime kumeneko.