Yoweli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+ Zefaniya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+ Machitidwe 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka.”’+
32 Ndiyeno aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+ pakuti m’phiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ monga mmene Yehova ananenera. Amenewa ndi anthu amene Yehova akuwaitana.”+
9 Pamenepo ndidzapatsa mitundu ya anthu chilankhulo choyera+ kuti onse aziitanira pa dzina la Yehova+ ndi kumutumikira mogwirizana.’*+