Yesaya 46:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.+ Chilungamocho sichili kutali,+ ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzam’patsa kukongola kwanga.”+ Obadiya 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu onse opulumuka adzakhala m’phiri la Ziyoni+ ndipo phiri limeneli lidzakhala loyera.+ A nyumba ya Yakobo adzatenga zinthu zoyeneradi kukhala zawo.+
13 Ine ndabweretsa pafupi chilungamo changa.+ Chilungamocho sichili kutali,+ ndipo chipulumutso changa sichidzachedwa.+ Ndidzapereka chipulumutso mu Ziyoni, ndipo Isiraeli ndidzam’patsa kukongola kwanga.”+
17 “Anthu onse opulumuka adzakhala m’phiri la Ziyoni+ ndipo phiri limeneli lidzakhala loyera.+ A nyumba ya Yakobo adzatenga zinthu zoyeneradi kukhala zawo.+