Yesaya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzatsale mu Yerusalemu adzakhala oyera kwa iye.+ Amenewa adzakhala anthu onse amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo mu Yerusalemu.+ Zekariya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”
3 Amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzatsale mu Yerusalemu adzakhala oyera kwa iye.+ Amenewa adzakhala anthu onse amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo mu Yerusalemu.+
3 “Yehova wanena kuti, ‘Ndidzabwerera ku Ziyoni+ ndipo ndidzakhala mu Yerusalemu.+ Yerusalemu adzatchedwadi mzinda wa choonadi+ ndi phiri loyera+ la Yehova+ wa makamu.’”