Yesaya 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aliyense amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzasiyidwe mu Yerusalemu adzatchedwa woyera, anthu onse a mu Yerusalemu amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:3 Yesaya 1, ptsa. 67-69
3 Aliyense amene adzatsale mu Ziyoni ndiponso amene adzasiyidwe mu Yerusalemu adzatchedwa woyera, anthu onse a mu Yerusalemu amene analembedwa mayina kuti akhale ndi moyo.+