Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 60:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+

  • Zekariya 14:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Anthu inu mudzathawira kuchigwa chimene chidzakhale pakati pa mapiri anga,+ chifukwa chakuti chigwacho chidzafika mpaka ku Azeli. Mudzathawa ngati mmene munachitira pothawa chivomezi chimene chinachitika m’masiku a Uziya, mfumu ya Yuda.+ Ndithu, Yehova Mulungu wanga adzabwera+ limodzi ndi oyera onse.+

  • Mateyu 23:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 kuti magazi onse olungama okhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu,+ kuyambira magazi a Abele+ wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena