Salimo 37:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma anthu ofatsa adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzasangalala ndi mtendere wochuluka.+ Salimo 37:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Olungama adzalandira dziko lapansi,+Ndipo adzakhala mmenemo kwamuyaya.+ Mateyu 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Odala ndi anthu amene ali ofatsa,+ chifukwa adzalandira dziko lapansi.+ Chivumbulutso 21:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+
7 Aliyense wopambana pa nkhondo adzalandira zimenezi monga cholowa. Ineyo ndidzakhala Mulungu wake,+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+