Ekisodo 32:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Komano ngati mukufuna kuwakhululukira tchimo lawo,+ . . . koma ngati simukufuna, ndifafanizeni+ chonde, m’buku lanu+ limene mwalemba.” Chivumbulutso 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho amene wapambana pa nkhondo+ adzavekedwa malaya akunja oyera.+ Ndipo sindidzafafaniza dzina lake m’buku la moyo,+ koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga,+ ndi pamaso pa angelo ake.+ Chivumbulutso 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Komanso, aliyense amene sanapezeke atalembedwa m’buku la moyo+ anaponyedwa m’nyanja yamoto.+
32 Komano ngati mukufuna kuwakhululukira tchimo lawo,+ . . . koma ngati simukufuna, ndifafanizeni+ chonde, m’buku lanu+ limene mwalemba.”
5 Choncho amene wapambana pa nkhondo+ adzavekedwa malaya akunja oyera.+ Ndipo sindidzafafaniza dzina lake m’buku la moyo,+ koma ndidzavomereza dzina lake pamaso pa Atate wanga,+ ndi pamaso pa angelo ake.+